Skip to main content
news Breaking News
clock

Pitani mukasake nokha mafuta – boma lathodwa

This article was originally published on Malawi24, Malawi's #1 independent news platform. Inde boma ndichimatchini ndipo chikafuna kuluma sichisewera: Koma kwapano khala ngati manu aguluka. Nalo lalema ndi vuto lakusowa kwa mafuta, mpaka lawuza kampani kuti zi...

Pitani mukasake nokha mafuta – boma lathodwa

This article was originally published on Malawi24, Malawi's #1 independent news platform.

Inde boma ndichimatchini ndipo chikafuna kuluma sichisewera: Koma kwapano khala ngati manu aguluka. Nalo lalema ndi vuto lakusowa kwa mafuta, mpaka lawuza kampani kuti ziwuyatse ulendo wa kunja zikasake zokha dizilo. Bungwe la Malawi Energy Regulatory Authority (MERA) lati tsopano lipereka chirolezo ku makampani omwe akugwira ntchito zazikulu zachitukuko kuti zipite kuli konse komwe zingathe […]

Read the full article and more Malawi news at Malawi24 — Breaking news, politics, business, sport and entertainment from Malawi and Africa, updated 24/7.

Read the full article at Malawi Nyasa

Article details
Published
November 17, 2026
Last updated
November 20, 2026
Written by
ADM Staff
Reading time
1 min read
Views
1
A
Written by

ADM Staff

Platform administrator at Afridev Monitor. Oversees the newsroom platform, user access and publishing settings, keeping the site reliable and editorially consistent. Afridev Monitor tracks development, policy and business news across Africa.

Leave a Reply

Cancel Reply

Your email address will not be published.

Please Accept Cookies for Better Performance