Skip to main content
news Breaking News
clock

Madobadobawa simudzawawonaso – Chisale

This article was originally published on Malawi24, Malawi's #1 independent news platform. Nanga angalime? Ayitu, madobadobawo ntchito ndiyomweyo. Komabe, kuyambira lero lolemba akuyenera kupeza dimba poti nduna yanenetsa kuti iwaonetsa chidameta nkhanga mpala....

Madobadobawa simudzawawonaso  – Chisale

This article was originally published on Malawi24, Malawi's #1 independent news platform.

Nanga angalime? Ayitu, madobadobawo ntchito ndiyomweyo. Komabe, kuyambira lero lolemba akuyenera kupeza dimba poti nduna yanenetsa kuti iwaonetsa chidameta nkhanga mpala. Wachiwiri kwa nduna yachitetezo mdziko, Norman Chisale walengeza kuti kuyambira lero lolemba, madobadoba omwe amapezeka ku maofesi a nthambi yopanga ziphaso zoyendera sadzapezekaso. Poyankhula loweruka, Chisale wati ena mwa mavuto omwe anthu akukumana nawo […]

Read the full article and more Malawi news at Malawi24 — Breaking news, politics, business, sport and entertainment from Malawi and Africa, updated 24/7.

Read the full article at Malawi Nyasa

Article details
Published
November 16, 2026
Last updated
November 20, 2026
Written by
ADM Staff
Reading time
1 min read
Views
1
A
Written by

ADM Staff

Platform administrator at Afridev Monitor. Oversees the newsroom platform, user access and publishing settings, keeping the site reliable and editorially consistent. Afridev Monitor tracks development, policy and business news across Africa.

Leave a Reply

Cancel Reply

Your email address will not be published.

Please Accept Cookies for Better Performance