This article was originally published on Malawi24, Malawi's #1 independent news platform.
Mwina akadadziwa Michael Usi adakangokhala osapereka maganizo ake pa momwe adindo angathanirane ndi mavuto a zachuma omwe akuta dziko lino, chifukwa nde wangodzikalasulira moto. Woyankhulira boma yemweso ndi nduna yofalitsa nkhani Shadric Namalomba, wasambwadza Usi, ndipo wamuuza kuti ngati akufuna apatsidweso udindo wa wachiwiri kwa m’tsogoleri wa dziko anene. Chatsitsa dzaye nchakuti Lolemba sabata ino, […]
Read the full article and more Malawi news at Malawi24 — Breaking news, politics, business, sport and entertainment from Malawi and Africa, updated 24/7.